Innocent Masina Nkhonyo


Comments about Innocent Masina Nkhonyo

  • Matthews Fatsani Chitha (7/20/2010 1:35:00 AM)

    I wouldn't hastate to appreciate what nkhonyo writes.I have been admiring this guy from the time i first met him at mlale seminary.He is multi-talented & i wouldn't manege to list what he does.All the best nkhonyo, am one those who are proud of you; keep it up!

    0 person liked.
    0 person did not like.

Za Kukhosi

MAGANIZO ANGA/ZA KUKHOSI

ZITHUNZIZO SIZAMANYADO CHABE NDI ZOTI MUDZAPONYERE VOTI

WOLEMBA: INNOCENT MASINA NKHONYO

“Inetu alamu ndikungofuna kachithunziko basi.” Mawuwatu amachokera kwa mayi wina amene anabwera kudzalembetsa nawo m’kaundula wa voti pa sukulu ya Kakule mum’zinda wa Lilongwe. Pa tsikuli nanenso ndinabwera pa sukuluyi ndi cholinga chomwecho. Nditamva ndemangayo ndinagwetsa nkhope yanga pasi, anandikhudza mawuwo. Ndinazindikira kuti pamene boma liri kalikiliki kupeza njira z

[Report Error]