Tidzayimba Poem by Chikondi Daniel Dziko

Tidzayimba

Nafe likudza tsiku tidzaimba
Nyimbo ya fuko, kuwala kutafika
Likudza tsiku ana anthu adzavina
Nyimbo zachimtali, kadzuwa kakulowa
Ndi nfuwu tidzaimba
Nyimbo yatspopano

Mbambadi likudza tsiku tidzaimba
Thungululu amayi zili pakamwa
Abambo akuponda ngoma
Fumbi la nzikili ndi honala lili kobo!
Likudza tsiku lidzafika
Ndipo pa tsikulo tidzaimba

Tidzayimba
Thursday, January 17, 2019
Topic(s) of this poem: change,political
POET'S NOTES ABOUT THE POEM
the poem is written in chechewa the language of mother malawi. It describes the day that will come when the dawn of change shall come on our country. that day people will rejoice
COMMENTS OF THE POEM
READ THIS POEM IN OTHER LANGUAGES
Close
Error Success