Denny Moonde

Veteran Poet - 1,246 Points (November 26th / Livingstone)

Muntu Wanga - Poem by Denny Moonde

Tifunseko.
Bushe muliko?
Odi kokoliko….
Mwaikumbuka nkoloko?
Tinaifaka maloko.
Patumba maboloko
Tifunseko.
Kodi muliko?
Muntu wanga
Pa street pa mita.
Pachitika mulomo
Tipisana ma pomo
Posiya kuvoka
Tikabila ku vota.
Muntu wanga
Zonse zaka zapita
Muti shinka butter
Tizamilizani kapata
Chikonko chanipata
Tifunseko,
Tamiwonani na nseko
Nase tisebenzeko
Segulani chiseko
Mwakula Mapapiko
Kuseni Tikawuka
Tipeze Wambululuka.
Nzi nzi nzi
Monga Inzi
Panjala Zingokugwa Minzi
Akuti Pa Zed ni zi
Tikujubani mu size
Timifake napa side
Kaili simumvela
Mweka kungomwela
Mwakula chimwela
Talema chikwela
Muntu wanga
Tikuchosa ganja
Tate sogolelani banja
Aka ka verse nika Pa Street
Tibwezeleni malaiti.
Mwaka uno nayo nayo tait
Machimo ni faiti

Topic(s) of this poem: social

Form: Free Verse


Poet's Notes about The Poem

Social

Comments about Muntu Wanga by Denny Moonde

There is no comment submitted by members..Read this poem in other languages

This poem has not been translated into any other language yet.

I would like to translate this poem »

word flags


Poem Submitted: Saturday, January 16, 2016

Poem Edited: Saturday, January 16, 2016


[Report Error]